Mateyu 25:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “Chotero khalanibe maso+ chifukwa simukudziwa tsiku kapena ola lake.+ Maliko 13:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Khalani maso, khalani tcheru,+ pakuti simukudziwa pamene nthawi yoikidwiratu idzafika.+ Luka 21:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Chotero khalani maso+ ndipo muzipemphera mopembedzera+ nthawi zonse, kuti mudzathe kuthawa zinthu zonsezi zimene zikuyembekezeka kuchitika. Kutinso mudzathe kuima pamaso pa Mwana wa munthu.”+
36 Chotero khalani maso+ ndipo muzipemphera mopembedzera+ nthawi zonse, kuti mudzathe kuthawa zinthu zonsezi zimene zikuyembekezeka kuchitika. Kutinso mudzathe kuima pamaso pa Mwana wa munthu.”+