Aefeso 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kudzera mwa iyeyu, tinamasulidwa ndi dipo* la magazi+ ake, inde, takhululukidwa+ machimo athu, malinga ndi chuma cha kukoma mtima kwake kwakukulu.+ Aheberi 9:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Inde, pafupifupi zinthu zonse zimayeretsedwa ndi magazi+ malinga ndi Chilamulo, ndipo popanda kukhetsa magazi+ anthu sangakhululukidwe machimo awo.+
7 Kudzera mwa iyeyu, tinamasulidwa ndi dipo* la magazi+ ake, inde, takhululukidwa+ machimo athu, malinga ndi chuma cha kukoma mtima kwake kwakukulu.+
22 Inde, pafupifupi zinthu zonse zimayeretsedwa ndi magazi+ malinga ndi Chilamulo, ndipo popanda kukhetsa magazi+ anthu sangakhululukidwe machimo awo.+