Luka 22:69 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 69 Koma kuyambira tsopano Mwana wa munthu+ adzakhala kudzanja lamanja+ lamphamvu la Mulungu.”+