Mateyu 26:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 n’kuwafunsa kuti: “Kodi mudzandipatsa chiyani ndikamupereka kwa inu?”+ Iwo anamulonjeza ndalama 30 zasiliva.+ Maliko 14:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Atamva zimenezo, iwo anasangalala ndi kumulonjeza kuti am’patsa ndalama zasiliva.+ Choncho iye anayamba kufunafuna mpata wabwino umene angamuperekere.+
15 n’kuwafunsa kuti: “Kodi mudzandipatsa chiyani ndikamupereka kwa inu?”+ Iwo anamulonjeza ndalama 30 zasiliva.+
11 Atamva zimenezo, iwo anasangalala ndi kumulonjeza kuti am’patsa ndalama zasiliva.+ Choncho iye anayamba kufunafuna mpata wabwino umene angamuperekere.+