Miyambo 11:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Munthu wopanda nzeru mumtima mwake amanyoza mnzake,+ koma munthu wozindikira bwino ndi amene amakhala chete.+ Yesaya 53:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Iye anapanikizidwa+ ndipo analola kuti asautsidwe,+ koma sanatsegule pakamwa pake. Anatengedwa ngati nkhosa yopita kokaphedwa,+ ndipo mofanana ndi nkhosa yaikazi imene imakhala chete akamaimeta ubweya, nayenso sanatsegule pakamwa pake.+ Mateyu 26:63 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 63 Koma Yesu anangokhala chete.+ Chotero mkulu wa ansembe anati: “Ndikukulumbiritsa pali Mulungu wamoyo,+ utiuze ngati ndiwedi Khristu+ Mwana wa Mulungu!” Yohane 19:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Analowanso m’nyumba ya bwanamkubwa ndi kufunsa Yesu kuti: “Kodi umachokera kuti?” Koma Yesu sanamuyankhe.+
12 Munthu wopanda nzeru mumtima mwake amanyoza mnzake,+ koma munthu wozindikira bwino ndi amene amakhala chete.+
7 Iye anapanikizidwa+ ndipo analola kuti asautsidwe,+ koma sanatsegule pakamwa pake. Anatengedwa ngati nkhosa yopita kokaphedwa,+ ndipo mofanana ndi nkhosa yaikazi imene imakhala chete akamaimeta ubweya, nayenso sanatsegule pakamwa pake.+
63 Koma Yesu anangokhala chete.+ Chotero mkulu wa ansembe anati: “Ndikukulumbiritsa pali Mulungu wamoyo,+ utiuze ngati ndiwedi Khristu+ Mwana wa Mulungu!”
9 Analowanso m’nyumba ya bwanamkubwa ndi kufunsa Yesu kuti: “Kodi umachokera kuti?” Koma Yesu sanamuyankhe.+