Mateyu 26:61 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 61 ndi kunena kuti: “Munthu ameneyu ananena kuti, ‘Ndikhoza kugwetsa kachisi wa Mulungu ndi kumumanganso m’masiku atatu.’”+ Yohane 2:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Yesu anawayankha kuti: “Gwetsani kachisi uyu,+ ndipo ine ndidzamumanga m’masiku atatu.”
61 ndi kunena kuti: “Munthu ameneyu ananena kuti, ‘Ndikhoza kugwetsa kachisi wa Mulungu ndi kumumanganso m’masiku atatu.’”+