Maliko 14:62 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 62 Pamenepo Yesu anati: “Inde ndinedi, ndipo anthu inu mudzaona Mwana wa munthu+ atakhala kudzanja lamanja+ lamphamvu. Mudzamuonanso akubwera ndi mitambo yakumwamba.”+ Yohane 5:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pa chifukwa chimenechi, Ayudawo anayamba kufunafuna njira yomuphera,+ chifukwa kuwonjezera pa kuphwanya Sabata, anali kunenanso kuti Mulungu ndi Atate wake,+ kudziyesa wofanana+ ndi Mulungu. Yohane 10:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 nanga kodi inu mukundiuza ine woyeretsedwa ndi Atate ndi kutumizidwa m’dziko kuti, ‘Ukunyoza Mulungu,’ chifukwa ndanena kuti, Ndine Mwana wa Mulungu?+
62 Pamenepo Yesu anati: “Inde ndinedi, ndipo anthu inu mudzaona Mwana wa munthu+ atakhala kudzanja lamanja+ lamphamvu. Mudzamuonanso akubwera ndi mitambo yakumwamba.”+
18 Pa chifukwa chimenechi, Ayudawo anayamba kufunafuna njira yomuphera,+ chifukwa kuwonjezera pa kuphwanya Sabata, anali kunenanso kuti Mulungu ndi Atate wake,+ kudziyesa wofanana+ ndi Mulungu.
36 nanga kodi inu mukundiuza ine woyeretsedwa ndi Atate ndi kutumizidwa m’dziko kuti, ‘Ukunyoza Mulungu,’ chifukwa ndanena kuti, Ndine Mwana wa Mulungu?+