Maliko 1:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Atapita patsogolo pang’ono, anaona Yakobo mwana wa Zebedayo, ndi m’bale wake Yohane, ali mu ngalawa yawo akusoka maukonde awo.+ Yohane 21:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Simoni Petulo, Tomasi wotchedwa Didimo,+ Natanayeli+ wa ku Kana wa m’Galileya, ana a Zebedayo,+ ndi ophunzira ake ena awiri anali pamodzi.
19 Atapita patsogolo pang’ono, anaona Yakobo mwana wa Zebedayo, ndi m’bale wake Yohane, ali mu ngalawa yawo akusoka maukonde awo.+
2 Simoni Petulo, Tomasi wotchedwa Didimo,+ Natanayeli+ wa ku Kana wa m’Galileya, ana a Zebedayo,+ ndi ophunzira ake ena awiri anali pamodzi.