Mateyu 11:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kuyambira m’masiku a Yohane M’batizi mpaka tsopano anthu akulimbikira kupeza mwayi wolowa mu ufumu wakumwamba, ndipo amene akulimbikira mwakhama akuupeza.+
12 Kuyambira m’masiku a Yohane M’batizi mpaka tsopano anthu akulimbikira kupeza mwayi wolowa mu ufumu wakumwamba, ndipo amene akulimbikira mwakhama akuupeza.+