Maliko 5:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Atalowa mkati, anafunsa anthuwo kuti: “N’chifukwa chiyani mukubuma ndi kulira motere? Mwana wamng’onoyu sanamwalire ayi, koma akugona.”+ Yohane 11:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Atanena zimenezi, kenako anauza ophunzira akewo kuti: “Bwenzi lathu Lazaro ali m’tulo akupumula, koma ndikupita kumeneko kukamudzutsa ku tulo take.”+
39 Atalowa mkati, anafunsa anthuwo kuti: “N’chifukwa chiyani mukubuma ndi kulira motere? Mwana wamng’onoyu sanamwalire ayi, koma akugona.”+
11 Atanena zimenezi, kenako anauza ophunzira akewo kuti: “Bwenzi lathu Lazaro ali m’tulo akupumula, koma ndikupita kumeneko kukamudzutsa ku tulo take.”+