1 Mafumu 17:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Chotero Eliya ananyamuka kupita ku Zarefati n’kulowa pachipata cha mzindawo. Kenako anaona mayi, mkazi wamasiye, akutola nkhuni. Ndiyeno anamuitana n’kumuuza kuti: “Undipatseko madzi pang’ono m’chikho kuti ndimwe.”+ 2 Mafumu 4:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Tsiku lina Elisa anapita ku Sunemu.+ Kumeneko kunali mayi wina wodziwika. Mayiyo anaumiriza+ Elisa kuti adye chakudya. Nthawi zonse Elisa akamadutsa, anali kupatukira kumeneko kukadya chakudya.
10 Chotero Eliya ananyamuka kupita ku Zarefati n’kulowa pachipata cha mzindawo. Kenako anaona mayi, mkazi wamasiye, akutola nkhuni. Ndiyeno anamuitana n’kumuuza kuti: “Undipatseko madzi pang’ono m’chikho kuti ndimwe.”+
8 Tsiku lina Elisa anapita ku Sunemu.+ Kumeneko kunali mayi wina wodziwika. Mayiyo anaumiriza+ Elisa kuti adye chakudya. Nthawi zonse Elisa akamadutsa, anali kupatukira kumeneko kukadya chakudya.