Maliko 2:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Tsopano nthawi inayake Yesu anali kudutsa m’munda wa tirigu pa tsiku la sabata. Akuyenda, ophunzira ake anayamba kubudula+ ngala za tirigu.+
23 Tsopano nthawi inayake Yesu anali kudutsa m’munda wa tirigu pa tsiku la sabata. Akuyenda, ophunzira ake anayamba kubudula+ ngala za tirigu.+