Miyambo 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 ukamazifunafuna ngati siliva,+ ndi kuzifufuza ngati chuma chobisika,+ Miyambo 8:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Chuma ndi ulemerero zili ndi ine.+ Ndilinso ndi cholowa chamtengo wapatali ndi chilungamo.+