Mateyu 20:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Aganyu amenewa atagwirizana nawo kuti aziwapatsa ndalama ya dinari imodzi pa tsiku,+ anawatumiza kumunda wake wa mpesa.
2 Aganyu amenewa atagwirizana nawo kuti aziwapatsa ndalama ya dinari imodzi pa tsiku,+ anawatumiza kumunda wake wa mpesa.