Mateyu 19:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Yesu anawayankha kuti: “Ndithu ndikukuuzani, Pa nthawi ya kulenganso zinthu, pamene Mwana wa munthu adzakhala pampando wachifumu waulemerero, inu amene mwatsatira ine mudzakhalanso m’mipando yachifumu 12, kuweruza mafuko 12 a Isiraeli.+ Maliko 10:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Iwo anamuyankha kuti: “Mutilole kuti mmodzi wa ife adzakhale kudzanja lanu lamanja, ndipo wina adzakhale kumanzere kwanu mu ulemerero wanu.”+
28 Yesu anawayankha kuti: “Ndithu ndikukuuzani, Pa nthawi ya kulenganso zinthu, pamene Mwana wa munthu adzakhala pampando wachifumu waulemerero, inu amene mwatsatira ine mudzakhalanso m’mipando yachifumu 12, kuweruza mafuko 12 a Isiraeli.+
37 Iwo anamuyankha kuti: “Mutilole kuti mmodzi wa ife adzakhale kudzanja lanu lamanja, ndipo wina adzakhale kumanzere kwanu mu ulemerero wanu.”+