Mateyu 12:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Kenako anatambasula dzanja lake ndi kuloza ophunzira ake, n’kunena kuti: “Ona! Mayi anga ndi abale anga!+ Aroma 8:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Amatero chifukwa amene anawadziwa choyamba+ anawasankhiratu+ kuti adzakhale ofanana+ ndi Mwana wake,+ kuti iye akhale woyamba kubadwa+ pakati pa abale ake ambiri.+ Aheberi 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pakuti onse, woyeretsayo ndi amene akuyeretsedwawo,+ amachokera kwa mmodzi.+ Pa chifukwa chimenechi, iye sachita manyazi kuwatcha “abale,”+
49 Kenako anatambasula dzanja lake ndi kuloza ophunzira ake, n’kunena kuti: “Ona! Mayi anga ndi abale anga!+
29 Amatero chifukwa amene anawadziwa choyamba+ anawasankhiratu+ kuti adzakhale ofanana+ ndi Mwana wake,+ kuti iye akhale woyamba kubadwa+ pakati pa abale ake ambiri.+
11 Pakuti onse, woyeretsayo ndi amene akuyeretsedwawo,+ amachokera kwa mmodzi.+ Pa chifukwa chimenechi, iye sachita manyazi kuwatcha “abale,”+