Mateyu 13:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Anawauzanso fanizo lina,+ kuti: “Ufumu wakumwamba uli ngati kanjere ka mpiru*+ kamene munthu anakatenga ndi kukabzala m’munda wake. Luka 13:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pamenepo anapitiriza kuti: “Kodi ufumu wa Mulungu uli ngati chiyani, ndiuyerekeze ndi chiyani?+
31 Anawauzanso fanizo lina,+ kuti: “Ufumu wakumwamba uli ngati kanjere ka mpiru*+ kamene munthu anakatenga ndi kukabzala m’munda wake.