Luka 8:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Koma atangotsika n’kufika kumtunda, anakumana ndi munthu wina waziwanda wochokera mumzindawo. Kwa nthawi yaitali ndithu, munthuyo anali kungokhala osavala, komanso sanali kukhala kunyumba, koma kumanda.+
27 Koma atangotsika n’kufika kumtunda, anakumana ndi munthu wina waziwanda wochokera mumzindawo. Kwa nthawi yaitali ndithu, munthuyo anali kungokhala osavala, komanso sanali kukhala kunyumba, koma kumanda.+