Yesaya 53:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iye adzaphuka ngati nthambi+ pamaso pa winawake, ndiponso ngati muzu m’dziko lopanda madzi. Alibe maonekedwe alionse apamwamba kapena okongola,+ ndipo maonekedwe ake si osiririka m’maso mwathu.+ 1 Akorinto 1:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 koma ife timalalikira za Khristu amene anapachikidwa.+ Kwa Ayuda, chimenechi ndi chinthu chokhumudwitsa+ ndipo kwa mitundu ina ndi kupusa.+
2 Iye adzaphuka ngati nthambi+ pamaso pa winawake, ndiponso ngati muzu m’dziko lopanda madzi. Alibe maonekedwe alionse apamwamba kapena okongola,+ ndipo maonekedwe ake si osiririka m’maso mwathu.+
23 koma ife timalalikira za Khristu amene anapachikidwa.+ Kwa Ayuda, chimenechi ndi chinthu chokhumudwitsa+ ndipo kwa mitundu ina ndi kupusa.+