56 Ndipo akangolowa m’midzi, kapena m’mizinda, kapena m’madera ozungulira alionse,+ anthu anali kukhazika odwala m’misika. Iwo anali kum’dandaulira kuti angogwira+ chabe ulusi wopota wa m’mphepete mwa malaya ake+ akunja. Ndipo anthu ambiri anaugwira ndi kuchira.+