Mateyu 16:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Tsopano atafika m’zigawo za Kaisareya wa Filipi, Yesu anafunsa ophunzira ake kuti: “Kodi anthu akumanena kuti Mwana wa munthu ndani?”+ Luka 9:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Nthawi inayake, pamene anali kupemphera payekha, ophunzira ake anafika kwa iye onse pamodzi. Ndiyeno iye anawafunsa kuti: “Kodi anthuwa akumati ine ndine ndani?”+
13 Tsopano atafika m’zigawo za Kaisareya wa Filipi, Yesu anafunsa ophunzira ake kuti: “Kodi anthu akumanena kuti Mwana wa munthu ndani?”+
18 Nthawi inayake, pamene anali kupemphera payekha, ophunzira ake anafika kwa iye onse pamodzi. Ndiyeno iye anawafunsa kuti: “Kodi anthuwa akumati ine ndine ndani?”+