Mateyu 10:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Aliyense wopulumutsa moyo wake adzautaya, ndipo wotaya moyo wake chifukwa cha ine adzaupeza.+ Mateyu 16:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Pakuti aliyense wofuna kupulumutsa moyo wake adzautaya, koma aliyense wotaya moyo wake chifukwa cha ine adzaupeza.+ Luka 9:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Pakuti aliyense wofuna kupulumutsa moyo wake adzautaya. Koma aliyense wotaya moyo wake chifukwa cha ine, adzaupulumutsa.+ Yohane 12:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Aliyense wokonda moyo wake akuuwononga, koma wodana ndi moyo wake+ m’dziko lino akuusungira moyo wosatha.+ Chivumbulutso 12:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Iwo anamugonjetsa+ chifukwa cha magazi a Mwanawankhosa,+ ndiponso chifukwa cha mawu a umboni wawo.+ Ndipo iwo sanaone kuti miyoyo yawo ndi yofunika,+ ngakhale pamene anali pa ngozi yoti akhoza kufa.
25 Pakuti aliyense wofuna kupulumutsa moyo wake adzautaya, koma aliyense wotaya moyo wake chifukwa cha ine adzaupeza.+
24 Pakuti aliyense wofuna kupulumutsa moyo wake adzautaya. Koma aliyense wotaya moyo wake chifukwa cha ine, adzaupulumutsa.+
25 Aliyense wokonda moyo wake akuuwononga, koma wodana ndi moyo wake+ m’dziko lino akuusungira moyo wosatha.+
11 Iwo anamugonjetsa+ chifukwa cha magazi a Mwanawankhosa,+ ndiponso chifukwa cha mawu a umboni wawo.+ Ndipo iwo sanaone kuti miyoyo yawo ndi yofunika,+ ngakhale pamene anali pa ngozi yoti akhoza kufa.