Mateyu 16:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Kodi munthu angapindulenji ngati atapeza zinthu zonse za m’dzikoli koma n’kutaya moyo wake?+ Kapena munthu angapereke chiyani chosinthanitsa+ ndi moyo wake? Luka 9:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Kunena zoona, kodi munthu angapindulenji ngati atapeza zinthu zonse za m’dzikoli koma iyeyo n’kudzivulaza kapena kutaya moyo wake?+
26 Kodi munthu angapindulenji ngati atapeza zinthu zonse za m’dzikoli koma n’kutaya moyo wake?+ Kapena munthu angapereke chiyani chosinthanitsa+ ndi moyo wake?
25 Kunena zoona, kodi munthu angapindulenji ngati atapeza zinthu zonse za m’dzikoli koma iyeyo n’kudzivulaza kapena kutaya moyo wake?+