Mateyu 17:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Ambuye, muchitire chifundo mwana wanga wamwamuna, chifukwa ndi wakhunyu ndipo akuvutika kwambiri. Amagwera pamoto kawirikawiri ndiponso amagwera m’madzi kawirikawiri.+ Luka 9:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Mzimu umam’gwira, ndipo mwadzidzidzi amafuula, kenako umam’tsalimitsa kwinaku akuchita thovu. Mzimu+ umenewu umamuvulaza kwambiri ndipo suchoka msanga.
15 “Ambuye, muchitire chifundo mwana wanga wamwamuna, chifukwa ndi wakhunyu ndipo akuvutika kwambiri. Amagwera pamoto kawirikawiri ndiponso amagwera m’madzi kawirikawiri.+
39 Mzimu umam’gwira, ndipo mwadzidzidzi amafuula, kenako umam’tsalimitsa kwinaku akuchita thovu. Mzimu+ umenewu umamuvulaza kwambiri ndipo suchoka msanga.