Miyambo 15:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kuyankha modekha kumabweza mkwiyo,+ koma mawu opweteka amayambitsa mkwiyo.+ Miyambo 16:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Mtima wa munthu wanzeru umamuchititsa kuti asonyeze kuzindikira ndi pakamwa pake,+ ndipo umachititsa milomo yake kutulutsa mawu okopa.+ Akolose 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Nthawi zonse mawu anu azikhala achisomo,+ okoma ngati kuti mwawathira mchere,+ kuti mudziwe mmene mungayankhire+ wina aliyense.
23 Mtima wa munthu wanzeru umamuchititsa kuti asonyeze kuzindikira ndi pakamwa pake,+ ndipo umachititsa milomo yake kutulutsa mawu okopa.+
6 Nthawi zonse mawu anu azikhala achisomo,+ okoma ngati kuti mwawathira mchere,+ kuti mudziwe mmene mungayankhire+ wina aliyense.