Mateyu 17:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Patapita masiku 6 Yesu anatenga Petulo, Yakobo ndi Yohane m’bale wake, n’kukwera nawo m’phiri lalitali kwaokhaokha.+
17 Patapita masiku 6 Yesu anatenga Petulo, Yakobo ndi Yohane m’bale wake, n’kukwera nawo m’phiri lalitali kwaokhaokha.+