Aroma 8:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Ndani adzasumira mlandu anthu a Mulungu ochita kusankhidwa?+ Mulungu ndiye amawayesa olungama.+ Aefeso 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Wachita zimenezi monga mmene anatisankhira+ kuti tikakhale ogwirizana ndi Yesuyo dziko lisanakhazikitsidwe,+ kuti tikakhale oyera ndi opanda chilema+ pamaso pa Mulungu m’chikondi.+
4 Wachita zimenezi monga mmene anatisankhira+ kuti tikakhale ogwirizana ndi Yesuyo dziko lisanakhazikitsidwe,+ kuti tikakhale oyera ndi opanda chilema+ pamaso pa Mulungu m’chikondi.+