Maliko 12:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Ndiyeno anakhala pansi moyang’anana ndi moponyamo zopereka+ ndipo anali kuona mmene khamu la anthu linali kuponyera ndalama moponya zoperekamo. Anthu ambiri olemera anali kuponyamo makobidi ambiri.+
41 Ndiyeno anakhala pansi moyang’anana ndi moponyamo zopereka+ ndipo anali kuona mmene khamu la anthu linali kuponyera ndalama moponya zoperekamo. Anthu ambiri olemera anali kuponyamo makobidi ambiri.+