Mateyu 24:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 “Tsopano phunzirani mfundo imeneyi pa fanizo ili la mkuyu: Nthambi yake yanthete ikaphuka ndi kuchita masamba, mumadziwa kuti dzinja lili pafupi.+ Maliko 13:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 “Tsopano phunzirani pa fanizo ili la mkuyu: Pamene nthambi yake yanthete yaphuka ndi kuchita masamba, mumadziwa kuti dzinja lili pafupi.+
32 “Tsopano phunzirani mfundo imeneyi pa fanizo ili la mkuyu: Nthambi yake yanthete ikaphuka ndi kuchita masamba, mumadziwa kuti dzinja lili pafupi.+
28 “Tsopano phunzirani pa fanizo ili la mkuyu: Pamene nthambi yake yanthete yaphuka ndi kuchita masamba, mumadziwa kuti dzinja lili pafupi.+