Mateyu 21:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Komabe, ngakhale kuti anali kufunafuna mpata wakuti amugwire, ankaopa khamu la anthu, chifukwa anthuwo anali kukhulupirira kuti iye ndi mneneri.+ Mateyu 26:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iwo anali kupangana+ zoti agwire Yesu mochenjera ndi kumupha. Maliko 14:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iwo nthawi zonse anali kunena kuti: “Tisadzamugwire pa chikondwerero, mwina anthu angadzachite chipolowe.”+ Luka 20:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Tsopano alembi ndi ansembe aakulu aja, pozindikira kuti iye anali kunena za iwo mufanizolo, anayesetsa kupeza mpata kuti amugwire ola lomwelo, koma anaopa anthu.+
46 Komabe, ngakhale kuti anali kufunafuna mpata wakuti amugwire, ankaopa khamu la anthu, chifukwa anthuwo anali kukhulupirira kuti iye ndi mneneri.+
2 Iwo nthawi zonse anali kunena kuti: “Tisadzamugwire pa chikondwerero, mwina anthu angadzachite chipolowe.”+
19 Tsopano alembi ndi ansembe aakulu aja, pozindikira kuti iye anali kunena za iwo mufanizolo, anayesetsa kupeza mpata kuti amugwire ola lomwelo, koma anaopa anthu.+