Chivumbulutso 19:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mngeloyo anandiuza kuti: “Lemba: Odala ndiwo amene aitanidwa+ ku phwando la chakudya chamadzulo la ukwati+ wa Mwanawankhosa.” Anandiuzanso kuti: “Awa ndi mawu oona a Mulungu.”+
9 Mngeloyo anandiuza kuti: “Lemba: Odala ndiwo amene aitanidwa+ ku phwando la chakudya chamadzulo la ukwati+ wa Mwanawankhosa.” Anandiuzanso kuti: “Awa ndi mawu oona a Mulungu.”+