1 Mafumu 21:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndiyeno mupeze anthu awiri+ opanda pake+ adzakhale patsogolo pake ndi kupereka umboni wotsutsana naye.+ Adzanene kuti, ‘Iwe watemberera Mulungu ndi mfumu!’+ Kenako mukamutulutse kunja ndi kum’ponya miyala kuti afe.”+ Salimo 35:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mboni zachiwawa zimaimirira.+Zimandifunsa zinthu zimene sindikudziwa.+
10 Ndiyeno mupeze anthu awiri+ opanda pake+ adzakhale patsogolo pake ndi kupereka umboni wotsutsana naye.+ Adzanene kuti, ‘Iwe watemberera Mulungu ndi mfumu!’+ Kenako mukamutulutse kunja ndi kum’ponya miyala kuti afe.”+