Miyambo 25:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Munthu wonenera mnzake umboni wonama ali ngati chibonga cha kunkhondo, lupanga, ndi muvi wakuthwa.+ Maliko 12:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pamenepo Yesu anati: “Perekani zinthu za Kaisara kwa Kaisara,+ koma zinthu za Mulungu muzizipereka kwa Mulungu.”+ Ndipo iwo anadabwa naye kwambiri.+
18 Munthu wonenera mnzake umboni wonama ali ngati chibonga cha kunkhondo, lupanga, ndi muvi wakuthwa.+
17 Pamenepo Yesu anati: “Perekani zinthu za Kaisara kwa Kaisara,+ koma zinthu za Mulungu muzizipereka kwa Mulungu.”+ Ndipo iwo anadabwa naye kwambiri.+