Mateyu 14:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pa nthawiyo Herode,* wolamulira chigawo, anamva za Yesu+ Maliko 6:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Tsopano izi zinamveka kwa Mfumu Herode,* chifukwa dzina la Yesu linamveka paliponse. Anthu anali kunena kuti: “Yohane m’batizi wauka kwa akufa, ndipo pa chifukwa chimenechi akuchita ntchito zamphamvu.”+
14 Tsopano izi zinamveka kwa Mfumu Herode,* chifukwa dzina la Yesu linamveka paliponse. Anthu anali kunena kuti: “Yohane m’batizi wauka kwa akufa, ndipo pa chifukwa chimenechi akuchita ntchito zamphamvu.”+