Yohane 12:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Poyamba ophunzira akewo sanazindikire zimenezi.+ Koma pamene Yesu analandira ulemerero,+ iwo anakumbukira kuti zimenezi zinalembedwa ponena za iye. Anakumbukiranso kuti anamuchitira zimenezi.+
16 Poyamba ophunzira akewo sanazindikire zimenezi.+ Koma pamene Yesu analandira ulemerero,+ iwo anakumbukira kuti zimenezi zinalembedwa ponena za iye. Anakumbukiranso kuti anamuchitira zimenezi.+