Machitidwe 2:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Tsiku ndi tsiku anali kusonkhana kukachisi mogwirizana.+ Analinso kuyenderana m’nyumba zawo ndi kudyera limodzi chakudya mosangalala+ ndiponso ndi mtima wofunitsitsa kugawana zinthu.
46 Tsiku ndi tsiku anali kusonkhana kukachisi mogwirizana.+ Analinso kuyenderana m’nyumba zawo ndi kudyera limodzi chakudya mosangalala+ ndiponso ndi mtima wofunitsitsa kugawana zinthu.