Mateyu 9:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma kuti mudziwe kuti Mwana wa munthu ali ndi mphamvu padziko lapansi zokhululukira machimo+ . . .” pamenepo anauza wakufa ziwalo uja kuti: “Nyamuka, tenga kabedi kakoka uzipita kwanu.”+ Maliko 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Ndikunena ndi iwe, Nyamuka, tenga machira akowa, uzipita kwanu.”+ Yohane 5:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yesu anati: “Nyamuka, nyamula machira akowa ndi kuyamba kuyenda.”+
6 Koma kuti mudziwe kuti Mwana wa munthu ali ndi mphamvu padziko lapansi zokhululukira machimo+ . . .” pamenepo anauza wakufa ziwalo uja kuti: “Nyamuka, tenga kabedi kakoka uzipita kwanu.”+