Mateyu 26:53 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 53 Kapena ukuganiza kuti sindingapemphe Atate wanga kuti anditumizire magulu ankhondo oposa 12 a angelo nthawi yomwe ino?+ Yohane 18:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma Yesu anauza Petulo kuti: “Bwezera lupangalo m’chimake.+ Kodi sindiyenera kumwa za m’kapu imene Atate wandipatsa,+ zivute zitani?”
53 Kapena ukuganiza kuti sindingapemphe Atate wanga kuti anditumizire magulu ankhondo oposa 12 a angelo nthawi yomwe ino?+
11 Koma Yesu anauza Petulo kuti: “Bwezera lupangalo m’chimake.+ Kodi sindiyenera kumwa za m’kapu imene Atate wandipatsa,+ zivute zitani?”