Mateyu 28:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Tsiku la sabata litatha, m’bandakucha wa tsiku loyamba la mlunguwo, Mariya Mmagadala ndi Mariya wina uja anabwera kudzaona manda.+ Maliko 16:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Choncho tsiku la sabata+ litapita, Mariya Mmagadala,+ Mariya mayi wa Yakobo, ndi Salome anagula zonunkhira kuti akapake thupi la Yesu.+ Luka 24:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Pa tsiku loyamba la mlungu, amayi aja analawirira m’mawa kwambiri kupita kumandako, atatenga zonunkhira zimene anakonza zija.+
28 Tsiku la sabata litatha, m’bandakucha wa tsiku loyamba la mlunguwo, Mariya Mmagadala ndi Mariya wina uja anabwera kudzaona manda.+
16 Choncho tsiku la sabata+ litapita, Mariya Mmagadala,+ Mariya mayi wa Yakobo, ndi Salome anagula zonunkhira kuti akapake thupi la Yesu.+
24 Pa tsiku loyamba la mlungu, amayi aja analawirira m’mawa kwambiri kupita kumandako, atatenga zonunkhira zimene anakonza zija.+