2 Atesalonika 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pa nthawi imeneyo adzabwezera chilango+ kwa anthu osadziwa Mulungu+ ndi kwa anthu osamvera uthenga wabwino+ wonena za Ambuye wathu Yesu.+ 1 Yohane 5:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Munthu amene wavomereza Mwana ndiye kuti ali ndi moyo umenewu ndipo amene sanavomereze Mwana wa Mulungu alibe moyo umenewu.+
8 Pa nthawi imeneyo adzabwezera chilango+ kwa anthu osadziwa Mulungu+ ndi kwa anthu osamvera uthenga wabwino+ wonena za Ambuye wathu Yesu.+
12 Munthu amene wavomereza Mwana ndiye kuti ali ndi moyo umenewu ndipo amene sanavomereze Mwana wa Mulungu alibe moyo umenewu.+