42 Ndiyeno kunabwera munthu wina kuchokera ku Baala-salisa.+ Iye anabweretsera+ munthu wa Mulungu woonayo mkate wa zipatso zoyambirira kucha,+ mitanda 20 ya mkate wa balere,+ ndi tirigu watsopano m’thumba lake. Choncho Elisa anati: “Gawira anthuwa kuti adye.”+