Yohane 8:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Poyankha Ayudawo anati: “Kodi tikamanena kuti, Ndiwe Msamariya+ ndipo uli ndi chiwanda,+ tikulakwitsa ngati?” Yohane 10:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ambiri a iwo anali kunena kuti: “Ameneyu ali ndi chiwanda+ ndipo ndi wamisala. N’chifukwa chiyani mukumumvetsera?”
48 Poyankha Ayudawo anati: “Kodi tikamanena kuti, Ndiwe Msamariya+ ndipo uli ndi chiwanda,+ tikulakwitsa ngati?”
20 Ambiri a iwo anali kunena kuti: “Ameneyu ali ndi chiwanda+ ndipo ndi wamisala. N’chifukwa chiyani mukumumvetsera?”