-
Luka 7:38Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
38 Atafika anagwada kumapazi kwake ndi kuyamba kulira, mwakuti anayamba kunyowetsa mapazi ake ndi misozi, kwinaku akupukuta mapaziwo ndi tsitsi la m’mutu mwake. Komanso anapsompsona mapazi akewo mwachikondi ndi kuwapaka mafuta onunkhirawo.
-