Yohane 13:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Popeza kuti Yudasi anali kusunga bokosi la ndalama,+ ena anali kuganiza kuti Yesu anali kumuuza kuti: “Ugule zofunikira zonse za chikondwerero,” kapena kuti apereke kenakake kwa osauka.+
29 Popeza kuti Yudasi anali kusunga bokosi la ndalama,+ ena anali kuganiza kuti Yesu anali kumuuza kuti: “Ugule zofunikira zonse za chikondwerero,” kapena kuti apereke kenakake kwa osauka.+