Miyambo 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Chifukwa mapazi awo amathamangira zoipa,+ ndipo iwo amafulumira kukakhetsa magazi.+ Luka 16:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Koma iye anamuuza kuti, ‘Ngati sakumvera Zolemba za Mose+ ndi Zolemba za aneneri, sangathekebe ngakhale wina atauka kwa akufa.’”
31 Koma iye anamuuza kuti, ‘Ngati sakumvera Zolemba za Mose+ ndi Zolemba za aneneri, sangathekebe ngakhale wina atauka kwa akufa.’”