Machitidwe 17:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Zotsatira zake, ena mwa iwo anakhala okhulupirira+ ndipo anagwirizana ndi Paulo ndi Sila.+ Ndipo khamu lalikulu la Agiriki opembedza Mulungu, ndi amayi ambiri olemekezeka anachitanso chimodzimodzi.
4 Zotsatira zake, ena mwa iwo anakhala okhulupirira+ ndipo anagwirizana ndi Paulo ndi Sila.+ Ndipo khamu lalikulu la Agiriki opembedza Mulungu, ndi amayi ambiri olemekezeka anachitanso chimodzimodzi.