Luka 12:50 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 50 Ndithudi pali ubatizo umene ndiyenera kubatizidwa nawo, ndipotu ndikuvutika kwambiri mumtima kufikira utatha!+ Luka 22:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 kuti: “Atate, ngati mukufuna, ndichotsereni kapu iyi. Komatu chifuniro chanu chichitike,+ osati changa.”+ Aheberi 5:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pamene anali munthu, Khristu anapereka mapemphero opembedzera ndi opempha,+ kwa amene anali wokhoza kumupulumutsa ku imfa. Anapereka mapempherowa mofuula+ komanso akugwetsa misozi, ndipo anamumvera chifukwa chakuti anali kuopa Mulungu.+
50 Ndithudi pali ubatizo umene ndiyenera kubatizidwa nawo, ndipotu ndikuvutika kwambiri mumtima kufikira utatha!+
42 kuti: “Atate, ngati mukufuna, ndichotsereni kapu iyi. Komatu chifuniro chanu chichitike,+ osati changa.”+
7 Pamene anali munthu, Khristu anapereka mapemphero opembedzera ndi opempha,+ kwa amene anali wokhoza kumupulumutsa ku imfa. Anapereka mapempherowa mofuula+ komanso akugwetsa misozi, ndipo anamumvera chifukwa chakuti anali kuopa Mulungu.+