Mateyu 26:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Inu mukudziwa kuti pasika achitika pakangopita masiku awiri,+ ndipo Mwana wa munthu aperekedwa kuti akapachikidwe.”+ Yohane 12:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Koma Yesu anawayankha kuti: “Nthawi yafika yakuti Mwana wa munthu alemekezedwe.+ Yohane 17:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Yesu atalankhula zinthu zimenezi, anakweza maso ake kumwamba+ ndi kunena kuti: “Atate, nthawi yafika, lemekezani mwana wanu, kuti mwana wanu akulemekezeni.+
2 “Inu mukudziwa kuti pasika achitika pakangopita masiku awiri,+ ndipo Mwana wa munthu aperekedwa kuti akapachikidwe.”+
17 Yesu atalankhula zinthu zimenezi, anakweza maso ake kumwamba+ ndi kunena kuti: “Atate, nthawi yafika, lemekezani mwana wanu, kuti mwana wanu akulemekezeni.+