Machitidwe 24:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ife tapeza kuti munthu uyu ndi wovutitsa kwabasi,+ ndipo akuyambitsa zoukira boma+ pakati pa Ayuda onse padziko lapansi kumene kuli anthu. Ndiponso ndi mtsogoleri wa gulu lampatuko wa Anazareti.+
5 Ife tapeza kuti munthu uyu ndi wovutitsa kwabasi,+ ndipo akuyambitsa zoukira boma+ pakati pa Ayuda onse padziko lapansi kumene kuli anthu. Ndiponso ndi mtsogoleri wa gulu lampatuko wa Anazareti.+