Machitidwe 9:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ali pa ulendo wakewo, anayandikira Damasiko. Mwadzidzidzi anangoona ngwee! kuwala kochokera kumwamba kutamuzungulira.+ Machitidwe 26:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma ndili mumsewu dzuwa lili pamutu, Inu mfumu, ndinaona kuwala koposa kunyezimira kwa dzuwa kochokera kumwamba kutandizungulira pamodzi ndi amene ndinali nawo pa ulendowo.+
3 Ali pa ulendo wakewo, anayandikira Damasiko. Mwadzidzidzi anangoona ngwee! kuwala kochokera kumwamba kutamuzungulira.+
13 Koma ndili mumsewu dzuwa lili pamutu, Inu mfumu, ndinaona kuwala koposa kunyezimira kwa dzuwa kochokera kumwamba kutandizungulira pamodzi ndi amene ndinali nawo pa ulendowo.+